Job 5:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma chibadwire munthu amangodzitengera mavuto yekha mosalephera, monga momwe sizilepherera mbaliwali kuulukira ku mlengalenga, kuchokera pa moto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma munthu abadwira mavuto, monga mbaliwali zikwera ziuluzika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komatu munthu amabadwira kuti azunzike monga momwe mbaliwali zimathethekera mlengalenga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma munthu abadwira mabvuto, Monga mbaliwali zikwera ziuluzika.