Job 5:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Achikhala ndinali ine, ndikadatembenukira kwa Mulungu, ndikadapereka mlandu wanga kwa Iye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ine ndikadafuna Mulungu, ndikadaikira mlandu wanga Mulungu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma ndikanakhala ine, ndikanamudandawulira Mulungu; ndikanapereka mlandu wanga kwa Iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ine ndikadafuna Mulungu, Ndikadaikira mlandu wanga Mulungu;