Job 5:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ntchito zake ndi zazikulu ndi zosamvetseka. Zodabwitsa zimene amachita ndi zosaŵerengeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene achita zazikulu ndi zosalondoleka, zinthu zodabwitsa zosawerengeka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amachita zozizwitsa zimene sizimvetsetseka, zodabwitsa zimene sizingatheke kuwerengedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amene acita zazikuru ndi zosalondoleka, Zinthu zodabwiza zosawerengeka.