Job 7:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Moyo wa munthu pa dziko lapansi ndi wa ntchito yakalavulagaga. Masiku ake ali ngati a munthu waganyu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi munthu alibe nkhondo kunja kuno? Kodi masiku ake sakunga masiku a wolembedwa ntchito?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi munthu sakhala ndi ntchito yowawa pa dziko lapansi? Kodi masiku ake sali ngati munthu waganyu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi munthu alibe nkhondo kunja kuno? Kodi masiku ace sakunga masiku a wolembedwa nchito?