Job 7:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Nchifukwa chake sindidzatseka pakamwa. Ndiyenera kulankhula, chifukwa kukhosi kwanga kuli nthumanzi. Ndiyenera kudandaula, chifukwa mumtima mwanga muli zoŵaŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero sindidzaletsa pakamwa panga; ndidzalankhula popsinjika mu mzimu mwanga; ndidzadandaula pakuwawa mtima wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Nʼchifukwa chake ine sindidzakhala chete; ndidzayankhula mopsinjika mtima, ndidzadandaula mowawidwa mtima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero sindidzaletsa pakamwa panga; Ndidzalankhula popsinjika mumzimu mwanga; Ndidzadandaula pakuwawa mtima wanga.