Job 7:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndatopa nawo moyo wanga, sindingakonde kukhala moyo nthaŵi zonse. Ingondisiyani, poti moyo wanga uli ngati mpweya chabe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinyansidwa nao moyo wanga; sindidzakhala ndi moyo chikhalire; mundileke; pakuti masiku anga ndi achabe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndatopa nawo moyo wanga; sindingakonde kukhala moyo nthawi zonse. Ndisiyeni ndekha pakuti moyo wanga ulibe tanthauzo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinyansidwa nao moyo wanga; sindidzakhala ndi moyo cikhalire; Mundileke; pakuti masiku anga ndi acabe.