Job 7:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja kapolo amalakalaka mthunzi, wantchito amayembekezera malipiro ake,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga kapolo woliralira mthunzi, monga wolembedwa ntchito ayembekezera mphotho yake,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga ngati kapolo wolakalaka mthunzi wa nthawi yamadzulo, kapena ngati munthu waganyu woyembekezera malipiro ake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga kapolo woliralira mthunzi, Monga wolembedwa nchito ayembekezera mphotho yace,