Job 7:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikamagona ndimafunsa kuti, ‘Kodi kucha liti?’ Koma usiku ndi wautali, sindigona tulo, ndimangoti sadabusadabu mpaka mbandakucha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndigona pansi, ndikuti, Ndidzauka liti? Koma usiku undikulira; ndipo ndimapalapata mpaka mbandakucha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikamagona ndimaganiza kuti, ‘Kodi kucha liti?’ Usikuwo umatalika ndipo sindigona tulo mpaka mmawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndigona pansi, ndikuti, Ndidzauka liti? koma usiku undikulira; Ndipo ndimapalapata mpaka mbanda kuca.