Job 8:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi anthu amvulazakalewo nkupanda kukuphunzitsa? Kodi iwo nkupanda kukuuza zinthu? Pajatu mau a akulu akoma akagonera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene aja sangakuphunzitse, ndi kukufotokozera, ndi kutulutsa mau a mumtima mwao?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi iwo sadzakulangiza ndi kukufotokozera? Kodi sadzakuwuza mawu ochokera pa zimene amazidziwa?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amene aja sangakuphunzitse, ndi kukufotokozera, Ndi kuturutsa mau a mumtima mwao?