Job 8:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Kodi gumbwa nkumera pa nthaka yopanda chinyontho? Nanga bango nkukondwa kumene kulibe madzi?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati gumbwa aphuka popanda chinyontho? Ngati manchedza amera popanda madzi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi bango nʼkumera pa nthaka yopanda chinyontho? Nanga mawango nʼkukula bwino popanda madzi?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati gumbwa aphuka popanda cinyontho? Ngati mancedza amera popanda madzi?