Job 8:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kulimba mtima kwake kumafooka, zimene amakhulupirira zili ngati ukonde wa kangaude.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kulimbika mtima kwake kudzathyoka, chikhulupiriro chake chikunga nyumba ya kangaude.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kulimba mtima kwake kumafowoka; zimene iye amadalira zili ngati ukonde wa kangawude.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kulimbika mtima kwace kudzatyoka, Cikhulupiriro cace cikunga nyumba ya tandaude.