Job 8:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amatsamira pa nyumba yake, koma nyumbayo si yolimba konse. Amaigwiritsa, komabe siikhalitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzatsamira nyumba yake, koma yosamlimbira; adzaiumirira koma yosakhalitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amatsamira ukonde wake, koma umaduka; amawugwiritsitsa koma sulimba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzatsamira nyumba yace, koma yosamlimbira; Adzaiumirira koma yosakhalitsa.