Job 8:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mutamchotsa pamalo pakepo, palibe ndi mmodzi yemwe angadziŵe kuti iyeyo anali pamenepo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akamuononga kumchotsa pamalo pake, padzamkana, ndi kuti, Sindinakuona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pamene yachotsedwa pamalo pakepo, pamalopo pamakana chomeracho ndi kuti, ‘Ine sindinakuonepo.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akamuononga kumcotsa pamalo pace, Padzamkana, ndi kuti, Sindinakuona.