Job 8:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Kodi udzakhala ukulankhulabe zoterezi mpaka liti? Mau akoŵa akungopita ngati mphepo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Udzanena izi kufikira liti? Ndipo mau a pakamwa pako adzakhala ngati namondwe kufikira liti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi udzakhala ukuyankhula zoterezi mpaka liti? Mawu ako ali ngati mphepo yamkuntho.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Udzanena izi kufikira liti? Ndipo mau a pakamwa pako adzakhala ngati namondwe kufikira liti?