Job 8:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndithu Mulungu sangamkane munthu wopanda cholakwa, komanso anthu olakwa Mulungu sangaŵathandize konse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taona, Mulungu sakana munthu wangwiro; kapena kugwiriziza ochita zoipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndithudi, Mulungu sakana munthu amene alibe cholakwa kapena kulimbikitsa anthu ochita zoyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taona, Mulungu sakana munthu wangwiro; Kapena kugwiriziza ocita zoipa.