Job 8:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amene amadana nawe adzachita manyazi, malo okhalako anthu oipa sadzaonekanso.” Yobe
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo akudana nawe adzavala manyazi; ndi hema wa oipa adzakhala kuli zii.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adani ako adzachita manyazi, ndipo malo okhalamo anthu oyipa sadzaonekanso.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo akudana nawe adzabvala manyazi; Ndi hema wa oipa adzakhala kuli zi.