Job 8:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kapena ana ako adamchimwira, nkuwona Mulungu adaŵalanga chifukwa cha zochimwa zaozo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chinkana ana ako anamchimwira Iye, ndipo anawapereka mwa kulakwa kwao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene ana ako anamuchimwira Mulungu, Iye anawapereka kuti alangidwe chifukwa cha tchimo lawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cinkana ana ako anamcimwira Iye, Ndipo anawapereka mwa kulakwa kwao;