Job 8:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati iwe uchita zimene Mulungu afuna, ngati upemba kwa Mphambe,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma ukafunitsitsa Mulungu, ndi kupembedza Wamphamvuyonse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma utayangʼana kwa Mulungu, ndi kudandaulira Wamphamvuzonse,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ukafunitsitsa Mulungu, Ndi kupembedza Wamphamvuyonse;