Job 8:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chiyambi chako chidzaoneka ngati chochepa, kuyerekeza ndi m'mene udzakhalira komaliza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chinkana chiyambi chako chinali chaching'ono, chitsiriziro chako chidzachuluka kwambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chiyambi chako chidzaoneka ngati chochepa koma chimaliziro chako chidzakhala chopambana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo cinkana ciyambi cako cinali cacing'ono, Citsiriziro cako cidzacuruka kwambiri.