Job 8:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ife ndife adzulodzuloli, sitidziŵa kanthu ai. Moyo wathu pa dziko lapansi uli ngati chithunzithunzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ife ndife adzulo, osadziwa kanthu, popeza masiku athu a pa dziko lapansi ndiwo ngati mthunzi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti ife ndife ana adzulodzuloli ndipo sitidziwa chilichonse, ndipo moyo wathu pa dziko lapansi uli ngati chithunzithunzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ife ndife adzulo, osadziwa kanthu, Popeza masiku athu a pa dziko lapansi ndiwo ngati mthunzi;