Job 9:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithu Mulungu akapita pafupi ndi ine, sindimuwona konse. Akandidutsa, ine sindimpenya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taona, Mulungu apita pali ine, koma sindimpenya; napitirira, koma osamzindikira ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akapita pafupi ndi ine sindingathe kumuona; akadutsa, sindingathe kumuzindikira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taona, Mulungu apita pali ine, koma sindimpenya; Napitirira, koma osamaindikira ine.