Job 9:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akamalanda zinthu, ndani angathe kumletsa? Ndani angathe kumufunsa kuti, ‘Mukuchita chiyani?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taona, akwatula, adzambwezetsa ndani? Adzanena naye ndani, Mulikuchita chiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati Iye alanda zinthu, ndani angathe kumuletsa? Ndani anganene kwa Iye kuti, ‘Mukuchita chiyani?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taona, akwatula, adzambwezetsa ndani? Adzanena naye ndani, Mulikucita ciani?