Job 9:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mulungu sabweza ukali wake, adaononga adani ake othandizana ndi Rahabu, chilombo choipa chija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu sadzabweza mkwiyo wake; athandizi odzikuza awerama pansi pa Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu sabweza mkwiyo wake; ngakhale gulu lankhondo la Rahabe linawerama pa mapazi ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu sadzabweza mkwiyo wace; Athandizi odzikuza awerama pansi pa Iye.