Job 9:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale ndikadamuitana, Iye nkuvomera, sindikhulupirira kuti akadamvadi mau angawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikadaitana, ndipo akadayankha Iye, koma sindikadakhulupirira kuti Iye wamvera mau anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale ndikanamuyitana ndipo Iye ndi kuvomera, sindikhulupirira kuti akanamva mawu angawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikadaitana, ndipo akadayankha Iye, Koma sindikadakhulupirira kuti Iye wamvera mau anga,