Job 9:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja amandikantha ndi mavuto onga mphepo yamkuntho, amandipweteka ndi mabala ambiri, popanda nchifukwa chomwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti andithyola ndi mkuntho, nachulukitsa mabala anga kopanda chifukwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye akanandikantha ndi mphepo yamkuntho, ndipo akanandipweteka popanda chifukwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti andityola ndi mkuntho, Nacurukitsa mabala anga kopanda cifukwa.