Job 9:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu sandilola kuti ndipume, koma amandichulukitsirachulukitsira zoŵaŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sandilola kuti ndipume, koma andidzaza ndi zowawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu sakanandilola kuti ndipumenso koma akanandichulukitsira zowawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sandilola kuti ndipume, Koma andidzaza ndi zowawa.