Job 9:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Inde, ndikudziŵa kuti zimenezi ndi zoona, koma nanga munthu angathe bwanji kukhala wolungama pamaso pa Mulungu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zoona, ndidziwa kuti chili chotero. Koma munthu adzakhala wolungama bwanji kwa Mulungu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Zoonadi, ndikudziwa kuti zimenezi ndi zoona. Koma munthu angathe bwanji kukhala wolungama pamaso pa Mulungu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zoona, ndidziwa kuti ciri cotero. Koma munthu adzakhala walungama bwanji kwa Mulungu?