Job 9:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndiye ndilibe mlandu, koma sindidziyenereza, moyo wanga ndimaunyoza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chinkana ndikhala wangwiro, sindidzisamalira mwini, ndipeputsa moyo wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngakhale ine ndili wosalakwa, sindidziyenereza ndekha; moyo wanga ndimawupeputsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cinkana ndikhala wangwiro, sindidzisamalira mwini, Ndipeputsa moyo wanga.