Job 9:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Palibe chabwino ai. Nchifukwa chake ndikuti, Mulungu amaononga anthu oipa ndi anthu abwino omwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuli chimodzimodzi monsemo, m'mwemo ndikuti Iye aononga wangwiro ndi woipa pamodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zonse nʼzofanana; nʼchifukwa chake ndikuti, ‘Iye amawononga anthu osalakwa ndi anthu oyipa omwe.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuli cimodzimodzi monsemo, m'mwemo ndikuti Iye aononga wangwiro ndi woipa pamodzi.