Job 9:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu akapereka dziko m'manja mwa anthu oipa, amaŵatseka maso anthu oweruza dzikolo. Ngati si Iyeyo wachita zimenezi, nanga nkukhala yani?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dziko lapansi laperekedwa m'dzanja la woipa; aphimba maso a oweruza ake. Ngati sindiye, pali yaninso?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene dziko lagwa mʼmanja mwa anthu oyipa Iye amawatseka maso anthu oweruza dzikolo. Ngati si Iyeyo, nanga ndani?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dziko lapansi laperekedwa m'dzanja la woipa; Aphimba maso a oweruza ace. Ngati sindiye, pali yaninso?