Job 9:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Masiku anga ndi othamanga kwambiri kupambana munthu waliŵiro. Masikuwo amapita, ine osaona zabwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsopano masiku anga afulumira kuposa wamtokoma; athawa osaona chokoma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Masiku anga ndi othamanga kwambiri kupambana munthu waliwiro; masikuwo amapita ine osaonapo zabwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsopano masiku anga afulumira kuposa wamtokoma; Athawa osaona cokoma.