Job 9:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amayenda ngati zombo zaliŵiro zapanyanja, ngati mphungu yogudukira nyama yoti idye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Apitirira ngati zombo zaliwiro; ngati mphungu igudukira chakudya chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amayenda ngati mabwato a njedza pa nyanja, ngati mphungu zothamangira nyama zoti zidye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Apitirira ngati zombo zaliwiro; Ngati mphungu igudukira cakudya cace.