Job 9:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwina ndinganene kuti, ‘Ndidzaiŵala madandaulo anga, nkhope yanga sidzakhalanso yachisoni, ndipo ndidzasangalala.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikati, Ndidzaiwala chondidandaulitsa, ndidzasintha nkhope yanga yachisoni, ndidzasekerera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼtanena kuti, ‘Ndidzayiwala madandawulo anga, ndidzasintha nkhope yanga ndipo ndidzasekerera,’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikati, Ndidzaiwala condidandaulitsa, Ndidzasintha nkhope yanga yacisoni, ndidzasekerera;