Job 9:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati ndine wolakwa ndithu, chabwinotu, zagwa zatha!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mlandu udzanditsutsa; potero ndigwire ntchito chabe chifukwa ninji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Popeza ndapezeka kale wolakwa ndivutikirenji popanda phindu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mlandu udzanditsutsa; Potero ndigwire nchito cabe cifukwa ninji?