Job 9:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zoona, Mulungu si munthu ngati ine, kuti ndingakangane naye, sindingathe kutsutsana naye pa mlandu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti sindiye munthu, monga ine, kuti ndimyankhe. Kuti tikomane mlandu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mulungu si munthu ngati ine kuti ndithe kumuyankha, sindingathe kutsutsana naye mʼbwalo la milandu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti sindiye munthu, monga ine, kuti ndimyankhe, Kuti tikomane mlandu.