Job 9:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Palibe mkhalapakati woti nkutiweruza aŵirife, woti nkugamula mlandu pakati pa Mulungu ndi ine.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Palibe wakutiweruza, wakutisanjika ife tonse awiri manja ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakanapezeka munthu wina kuti akhale mʼkhalapakati wathu, kuti atibweretse ife tonse pamodzi,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Palibe wakutiweruza, Wakutisanjika ife tonse awiri manja ace.