Job 9:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero ndidakatha kulankhula osamuwopa, koma monga zilirimu, sindingathe konse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti ndinene, osamuopa, pakuti sinditero monga umo ndili.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo ine ndikanatha kuyankhula mosamuopa Mulunguyo, koma monga zililimu, sindingathe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti ndinene, osamuopa, Pakuti sinditero monga umo ndiri.