Job 9:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu ndi wanzeru, ndipo ndi wamphamvu kwambiri. Palibe munthu amene angathe kulimbana naye, popanda kupwetekerapo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiye wa mtima wanzeru, ndi wa mphamvu yaikulu; ndaniyo anadziumitsa mtima pa Iye, nakhala nao mtendere?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu ndi wa nzeru zambiri ndipo mphamvu zake ndi zochuluka. Ndani analimbana naye popanda kupwetekeka?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiye wa mtima wanzeru, ndi wa mphamvu yaikuru; Ndaniyo anadziumitsa mtima pa Iye, nakhala nao mtendere?