Joel 1:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tayani mtima, inu alimi, lirani, inu olima mphesa, chifukwa tirigu ndi barele, ndi zonse zam'minda zalephera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Gomani, akulima m'minda inu; lirani, akulima mpesa; chifukwa cha tirigu ndi barele; pakuti dzinthu za m'minda zatayika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Khalani ndi nkhawa, inu alimi, lirani mofuwula inu alimi a mphesa; imvani chisoni chifukwa cha tirigu ndi barele, pakuti zokolola za mʼmunda zawonongeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Gomani, akulima m'minda inu; lirani, akulima mpesa; cifukwa ca tirigu ndi barele; pakuti dzinthu za m'minda zatayika.