Joel 1:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mpesa wauma, mkuyu wafota. Mkangaza, kanjedza, mitengo ya apulosi ndi mitengo yonse ya m'dziko yaumiratu. Choncho chikondwerero cha anthu chatheratu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mpesa wauma, mkuyu wafota, mtengo wa mkangaza ndi kanjedza ndi muula, inde mitengo yonse ya kuthengo yafota; pakuti chimwemwe chathera ana a anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mpesa wauma ndipo mtengo wamkuyu wafota; makangadza, kanjedza ndi mitengo ya apulosi, mitengo yonse ya mʼmunda yauma. Ndithudi chimwemwe cha anthu chatheratu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mpesa wauma, mkuyu wafota, mtengo wa mkangaza ndi kanjedza ndi muula, inde mitengo yonse ya kuthengo yafota; pakuti cimwemwe cathera ana a anthu.