Joel 1:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kalanga ine! Tsiku loopsa layandikira, tsiku la Chauta, likubwera ndi chiwonongeko chochokera kwa Mphambe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kalanga ine, tsikuli! Pakuti layandikira tsiku la Yehova, lidzafika ngati chionongeko chochokera kwa Wamphamvuyonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kalanga ine tsikulo! Pakuti tsiku la Yehova layandikira; lidzabwera ngati chiwonongeko chochokera kwa Wamphamvuzonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kalanga ine, tsikuli! pakuti layandikira tsiku la Yehova, lidzafika ngati cionongeko cocokera kwa Wamphamvuyonse.