Joel 1:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chakudya chathu chikutha ife tikuwona. Mulibenso chimwemwe ndi chisangalalo m'Nyumba ya Mulungu wathu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chakudya sichichotsedwa kodi pamaso pathu? Chimwemwe ndi chikondwerero pa nyumba ya Mulungu wathu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi chakudya chathu sichachotsedwa ife tikuona? Kodi mʼnyumba ya Mulungu wathu simulibe chimwemwe ndi chisangalalo?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cakudya sicicotsedwa kodi pamaso pathu? cimwemwe ndi cikondwerero pa nyumba ya Mulungu wathu?