Joel 1:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu akuluakulu, mverani. Tcherani khutu, inu nonse okhala m'dziko. Kodi zoterezi zidaonekapo nthaŵi yanu kapena nthaŵi ya makolo anu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Imvani ichi, akuluakulu inu, nimutchere khutu, inu nonse okhala m'dziko. Chachitika ichi masiku anu kodi, kapena masiku a makolo anu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu akuluakulu, imvani izi; mvetserani, nonse amene mumakhala mʼdziko. Kodi zinthu zokhala ngati izi zinayamba zaonekapo mʼnthawi yanu, kapena mʼnthawi ya makolo anu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Imvani ici, akulu akulu inu, nimuchere khutu, inu nonse okhala m'dziko. Cacitika ici masiku anu kodi, kapena masiku a makolo anu?