Joel 1:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chikhamu cha dzombe chagwa m'dziko lathu nchamphamvu ndiponso chosaŵerengeka. Mano ake ali ngati a mkango wamphongo, zibwano zake ngati za mkango waukazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mtundu wadza, wakwerera dziko langa, wamphamvu wosawerengeka, mano ake akunga mano a mkango, nukhala nao mano achibwano a mkango waukulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtundu wa anthu wathira nkhondo dziko langa, wamphamvu ndi wosawerengeka; uli ndi mano a mkango, zibwano za mkango waukazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mtundu wadza, wakwerera dziko langa, wamphamvu wosawerengeka, mano ace akunga mano a mkango, nukhala nao mano acibwano a mkango waukuru.