Joel 1:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu anthu, lirani kwambiri ngati namwali wovala chiguduli. Wolira chifukwa cha imfa ya mnyamata wofuna kumkwatira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Lirani ngati namwali wodzimangira m'chuuno chiguduli, chifukwa cha mwamuna wa unamwali wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lirani ngati namwali wovala chiguduli, chifukwa cha mwamuna wa utsikana wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lirani ngati namwali wodzimangira m'cuuno ciguduli, cifukwa ca mwamuna wa unamwali wace.