Joel 1:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chopereka cha chakumwa ndi cha chakudya siziperekedwanso ku Nyumba ya Chauta. Ansembe akulira, atumiki a Chauta aja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nsembe yaufa ndi nsembe yothira zalekeka kunyumba ya Yehova; ansembe, atumiki a Yehova, achita maliro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chopereka cha chakudya ndi cha chakumwa sizikuperekedwa ku nyumba ya Yehova. Ansembe akulira, amene amatumikira pamaso pa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nsembe yaufa ndi nsembe yothira zalekeka ku nyumba ya Yehova; ansembe, atumiki a Yehova, acita maliro.