Joel 2:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dziko lapansi likugwedezeka pamene iwo akuyandikira. Mlengalenga ukunjenjemera. Dzuŵa ndi mwezi zikuchita mdima, ndipo nyenyezi zikuleka kuŵala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dziko lapansi linjenjemera pamaso pao, thambo ligwedezeka, dzuwa ndi mwezi zada, ndi nyenyezi zibweza kuwala kwao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Patsogolo pawo dziko limagwedezeka, thambo limanjenjemera, dzuwa ndi mwezi zimachita mdima, ndipo nyenyezi zimaleka kuwala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dziko lapansi linjenjemera pamaso pao, thambo ligwedezeka, dzuwa ndi mwezi zada, ndi nyenyezi zi'bweza kuwala kwao;