Joel 2:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo chikondi cha Chauta chidayaka ngati moto chifukwa cha dziko lake, ndipo adaŵachitira chifundo anthu ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Yehova anachitira dziko lake nsanje, nachitira anthu ake chifundo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Yehova adzachitira nsanje dziko lake ndi kuchitira chisoni anthu ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Yehova anacitira dziko lace nsanje, nacitira anthu ace cifundo.