Joel 2:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudzadziŵa kuti Ine ndili naye Israele, ndipo kuti Ine ndekha, osati wina, ndine Chauta, Mulungu wanu. Anthu anga sadzaŵanyozanso ai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mudzadziwa kuti Ine ndili pakati pa Israele, ndi kuti Ine ndine Yehova Mulungu wanu, palibe wina; ndi anthu anga sadzachita manyazi nthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo inu mudzadziwa kuti Ine ndili mu Israeli, kuti Ine ndine Yehova Mulungu wanu, ndi kuti palibenso wina; ndipo anthu anga sadzachitanso manyazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mudzadziwa kuti Ine ndiri pakati pa Israyeli, ndi kuti Ine ndine Yehova Mulungu wanu, palibe wina; ndi anthu anga sadzacita manyazi nthawi zonse.