Joel 2:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a mitundu ina amachita mantha akaŵaona, nkhope zonse zimatumbuluka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamaso pao mitundu ya anthu ikumva zowawa, nkhope yonse zitumbuluka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akangowaona, anthu a mitundu ina amazunzika mu mtima; nkhope iliyonse imagwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamaso pao mitundu ya anthu ikumva zowawa, nkhope zonse zitumbuluka.